Michael Usi ndi mtsogoleri amene dziko likanathandizidwa nayo, koma ndilosakonzeka kuti alisogolele

Via Times Exclusive

Anthu ambiri mumangopanga nsanje ndi kaduka. Koma apapa tayankhulani za chilungamo ndithu, wanenapo chani choti si chowona?

Reply